Agoloso ali ready kudzakusangalatsani pa 19 December 2025, Ku M-Cinema yomwe ili pa Chichiri Shopping Mall, Near Game stores Car Park.
M-Cinema ndi venue Yokongola kwambiri, ndipo anthu ali serious dzikoli.
Gulani ticket yanu pogwiritsa ntchito link yomwe ili m'musiyi. Kapena mukhoza kukagula nokha Manual pa Nkhungudzu Bookshop yomwe ili Mtauni ya Blantyre, Pa Kandodo Corner Shop, moyang'anizana ndi Engen Filling Station,